MSOSA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MSOSA, 12 Diesel Road, Kempton Park.

R400 inch free delivery San Msosa
14/03/2026

R400 inch free delivery San Msosa

28/01/2026

KUBWEZA NDATA NGATI MULI NDI UNA WAUKULU.

-Mchere plus mandimu mu madzi orzidzira.
KAPANGIDWE
Finyirani ndimu limodzi, table spoon imodzi ya kitchen salt, mu madzi orzidzira. Takasani bwinobwino ndikumatawasira kawiri pasiku ndipo kumabwerera kwa nthawi yochepa komanso ngati muli ndi mauka oti angoyamba kumene amabalalika of course madziwo akakumana ndi mauka aja kumawawa koma zimasiya kwa masiku ochepa. Pangani izi mpaka mutakhutisidwa kuti kwachepa molingana ndi katundu amene amalowa ku una kwanuko.

GUAVA LEAVES
Wilitsani masamba amagwafa okwanira chikatho chimoezi mu 1litre yamadzi.thirani mu pelo akadafunda, nthuzi ilipo ndipo khalirani peloyo kwa 15 to 20 minutes kenako chokanipo. Kamodzi pa tsiku kwa one week, ndipo mudzakhala virgin kachikenanso.

MASAMBA A MTENGO WA LILIME LA NG'OMBE
Mtengo uwu ndi wachilengedwe ndipo umapezeka mu phiri, tengani masamba akewo anyale pang'ono ndipo sinjani limodzi ndi sugar was brown. Zithirani mu phala kwinaku mukuvalira, mumabwereranso chikale komanso kutenthera bwino. Mwamuna amamva tseketseke ndithu.

MASAMBA A BWEMBA.

Ayanokeni pa mthuzi, akawuma ndi mphepo sinjani mix brown sugar then mizimwera ku phala komanso kuvalira. Kumabwereranso mosabvuta komanso ndatha amakhala wokoma sizinawoneke. Zikomo kwambiri ma comment anu akumandilimbikitsa kwambiri komanso ndimafuna nonse muli ma friends anga.

28/01/2026

If girls cheat on soldiers people..
what about you yohane
with your laptop bag
😏😂

🎙 Purezidenti wa Russia Vladimir Putin adachita msonkhano wogwira ntchito ndi mamembala okhazikika a Security Council of...
22/01/2026

🎙 Purezidenti wa Russia Vladimir Putin adachita msonkhano wogwira ntchito ndi mamembala okhazikika a Security Council of the Russian Federation pa Januware 21, 2026.

💬 Vladimir Putin: Ponena za US

Adona ali apawa akupanga trend ku South Africa chifukwa kanema wawo akuwinjidwa ndi mkulu ali kumanjayo, after kumunamiz...
17/01/2026

Adona ali apawa akupanga trend ku South Africa chifukwa kanema wawo akuwinjidwa ndi mkulu ali kumanjayo, after kumunamiza mkaziyo kuti ali ndi modelling agency ndipo amulemba ntchito, akuyenda kwambiri kumeneko.
Akufuna full Vidio Hala me +27704370935

100% natural honey with proof
17/01/2026

100% natural honey with proof

Address

12 Diesel Road
Kempton Park

Telephone

+27704370935

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MSOSA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MSOSA:

Share