Griv mwale

Directions

Griv mwale Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Griv mwale, Ntchisi.

nayeso Jomo ndi munthu amakwiya 😂😂😂😂 zilikotu ziliko
28/10/2026

nayeso Jomo ndi munthu amakwiya 😂😂😂😂 zilikotu ziliko

ichi chitangokhala chi tanker Cha petrol bwanj osati water Bowser 😂😂😂.madzi tikumwa amu tanker ngati petroleum😂😂😂
28/10/2026

ichi chitangokhala chi tanker Cha petrol bwanj osati water Bowser 😂😂😂.madzi tikumwa amu tanker ngati petroleum😂😂😂

koma Gangati iweyo anakoza.you are coming in strong with power🤣🤣🤣
27/10/2026

koma Gangati iweyo anakoza.you are coming in strong with power🤣🤣🤣

komatu JB iweyo ohooooooo!!!!!
27/10/2026

komatu JB iweyo ohooooooo!!!!!

ziliko2 ziliko.mpaka galimoto ya chipani kukhala pa mzere wa mafuta
26/10/2026

ziliko2 ziliko.mpaka galimoto ya chipani kukhala pa mzere wa mafuta

ndiye mwati featuring yanji iyi wina osaikamo verse??  koma2 ku music industry ku mutionetsa zinthu🤣🤣🤣.umakwana phyzo
22/10/2026

ndiye mwati featuring yanji iyi wina osaikamo verse?? koma2 ku music industry ku mutionetsa zinthu🤣🤣🤣.umakwana phyzo

mwati zikukhala bwanj ku ntchisi 😭😭
21/10/2026

mwati zikukhala bwanj ku ntchisi 😭😭

ambuye ndioneni.amnzanga Ali ku show ya crispy Malawi ndi 6th.ine ndili mu library  kuphaya. ndikungofuna mundione 1 MIT...
15/10/2026

ambuye ndioneni.amnzanga Ali ku show ya crispy Malawi ndi 6th.ine ndili mu library kuphaya. ndikungofuna mundione 1 MITA basi 😂😂😂😂

mwaionela kale ya achina
13/10/2026

mwaionela kale ya achina

11/10/2026

mmmmm amwene, zafika pakuti petulo akungopezeka mu baibulo mokha. ma filing station muli mbuuuuu 😂😂😂

Address

Ntchisi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Griv mwale posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Nearby grocery stores