09/06/2026
World Cup ya chaka Chino akusewelera ku America ndi maiko oyandikana....nde ma time zone awo ndiosiyana ndi kuno....so ma game ena aziyamba 1am ena azisewera 2days nde tikachoka Monday kubwera Friday muzitimvetsa tizikhala kuti tinali koonera world cup ndi anzathu!!
Zikomo!