CAST IRON Ernest chatepa

CAST IRON Ernest chatepa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from CAST IRON Ernest chatepa, Grocers, Cast iron@chatepa, Lilongwe.

03/12/2021

Amene muli kumademo kumpoto plz tapotananu pitani ochuluka ndithu born amuuza kuti udindo samupatsa komano boma langotsitsa zinthu zomwe zakwelazi komano udindo born sapatsidwa nde tikudziwa tonse kuti chiyambi chankhaniyi chinali choti akufuna udindo m,boma nde tiyeni tionetse kusakondwa inde zinthu zitsika komano born unduna amupatseπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

24/11/2021

Koma amalawi tamapolani moto moti 5pn ya pepala limodziyija ikulembedwa nchichewa? Tsono nanga bwanji mwaipatsa dzina la ochewa? Munvekele chi KWANTELE, KWANTELETELE,πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚koma muli nchipongwekkkkkkkk

23/11/2021

Ndimapita ku lilongwe kuchoka ku Blantyre ndafika pa manjawila ndati ndidzele chidule ndizembe toll gate ndalowa nsewu wa ntonda koma abale ndafika pa matale post office ndapeza mateyala andiuza kuti lipila 1pn ukudutsa nsewu wathu kkkkkkk kufika pakanzati ndapezapo Ana ajele aika masamba komanso matayala Ali mukudutsa nsewu wathu bambo tichuneniinayeke 1pn yagwanso pamenepa kukafika pa gwauya pa school ndapezanso anyata atchinganso nsewu andilipitsanso 1pn ati ukudutsa nsewu wathu ndakafika mwazililongwe andimanso kuona matayala akuti titchuleni angoni mukudutsa nseu watch kkkkkkk mmene ndimakafika ba benvu turn off nditaonaonga ndlama yopitilila 5pn kumatinso bola ndikadadadutsa toll gate yomweija ndikanangofapo 3pn kkkkkkk koma angoni akwaphambala ndi kwa champiti,anakonza,🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣

18/11/2021

Chipani Cha UTM chasankha MLAKA MALILO kuti akhale mtsogoleli wa achinyata kuchipani potengela kutula pansi kwa mrBORN KALINDO pa udindowu

18/11/2021

When you announce that you quit the party you belong and say your no longer a member of that party at the same time ten members show interest on your sit as party DOY mpamene umadzadziwa kuti izi ndi zandale si za ambuye, ikachoka imodzi mundale hundreds zimabwela,koma ikachoka imodzi mumpingo ndimasiya zinazo nkukaisaka Mr born be careful πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Cast Iron@chatepa
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CAST IRON Ernest chatepa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category