Moses Mavidi

Moses Mavidi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Moses Mavidi, Grocers, Soche, Blantyre.

18/03/2026

Kodi mukuziwa
death penalty

23/12/2025

get to know your phone

Pangani like kuti muziwe zambiri

10/12/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rollin Summerr, Stella Bwenzi, Mahfuz Khan, Ekra Adrien, Desper MW, Mw Lantos

08/12/2025

get to know your phone
ngat mukufuna kuti munthu yemwe alibe number yanu kapena sanaseve mukamuyimbila izilemba kuti private number komaso ngat munthu anakupanga block ngat ukufuna kuti umuyimbile kupanga kwake timatele

06/12/2025

kuziwa phone yanu

11/11/2025
Akuti ku India, bambo uyu, amamutcha Baba watutumutsa anthu.Baba ndi chiledzelere, usiku uliwonse amadzandira kuchoka ku...
26/10/2025

Akuti ku India, bambo uyu, amamutcha Baba watutumutsa anthu.

Baba ndi chiledzelere, usiku uliwonse amadzandira kuchoka kumowa kumapita kwawo.

Baba anawoneka pa cctv ya mu mseu akudzandila. Anawona Tiger pamseu.

Chodabwitsa ndichakuti, Baba anapita panali Tiger nkumamusisita.
Akuti Tiger anangomuchokera sanamulume.

Ena akuwona ngati chifukwa cha mowa, Baba ankayesa ngati mphaka.

Sidenote
Fisi anakana msatsi

Beautiful girl  🔥🔥
26/10/2025

Beautiful girl 🔥🔥

Yonse-bo
15/09/2025

Yonse-bo

Address

Soche
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Moses Mavidi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category