Ulimi wa tomato

Ulimi wa tomato Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ulimi wa tomato, Grocers, Dowa jonas, Lumbadzi.

Aka ndi kambozi komwe kamatcedw kuti nyaika kamavuta kwambili miyezi yomwe vula yasiila mpaka kudzabwelaso kwa vula kali...
22/04/2026

Aka ndi kambozi komwe kamatcedw kuti nyaika kamavuta kwambili miyezi yomwe vula yasiila mpaka kudzabwelaso kwa vula kali ndi kuthekela koti tomato akanika nanga kuthana nazo kwake tingatani?
1 kuthilila kawili kawili
2 mankhwala
.snow tiger/power tiger
.snow mectin/profex super
3 kuthana ndi ti agulugufe
.shooter
mukatelo tomato wanu mwakoza pamenepo. SHARE AND FOLLOW WA TOMATO

15/04/2026

tomato kwanuko ali pa bwanj nanga ndikuti?

ngati tomato wanu akuoneka chonchi pezani mankhal awa dimothreat ,dithane,blavo mukatel muthana naz imakhala mphepo imen...
28/02/2026

ngati tomato wanu akuoneka chonchi pezani mankhal awa dimothreat ,dithane,blavo mukatel muthana naz imakhala mphepo imeney .folliw ulimi wa tomato

24/02/2026

tapanga gulu la wap komwe tiziphuzitsana kasamalidw ka tomato,mbeu yoenela kudzala molingana ndi nyengo komaso kudziwitsana ntundu wa matenda atomato ndi makhwala ake.ponyani ma nambala tikupangen add pangani ulimi wa tomato komaso share post kuti azanu apange nawo

20/01/2026

mbewu ya tomato koma tangeru 97 ndi mashine pangan follow wa tomato kuti muphuzile zambili za tmato

Address

Dowa Jonas
Lumbadzi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ulimi wa tomato posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category