OSMAN & Family Investment

OSMAN & Family Investment This shop located in Liwonde township ,Machinga ,Malawi.

Chi Get 2 gather amwene. Pa 1st November pano kopita ndi ukuku insha Allah.
30/10/2026

Chi Get 2 gather amwene. Pa 1st November pano kopita ndi ukuku insha Allah.

Kodi ndi ntchimo? Film ina ikutuluka Mawa 6:00 PM In Shaa Allah Mwadikila nthawi yaitali, now the wait is over, get read...
30/10/2026

Kodi ndi ntchimo? Film ina ikutuluka Mawa 6:00 PM In Shaa Allah
Mwadikila nthawi yaitali, now the wait is over, get ready.

Inde chipembedzo nchokoma ndithu and chisilamu sichisekelela zili zonse how msilamu angapange promote zinthu za haram li...
29/10/2026

Inde chipembedzo nchokoma ndithu and chisilamu sichisekelela zili zonse how msilamu angapange promote zinthu za haram like juga, bet.

Tawaonapo akatswiri angapo otchuka akukana kupanga promote zinthu zomwe zili zolesedwa kuchipembezo chawo, chisanzo che mandota ananena kuti sazapezeka akupanga acting mu nyimbo za chikunja, tawaonapo osewera mpira ena ochokera mmaiko akunja akukana kuvala ma Jersey omwe akupanga promote za betting, manthanyula and mowa ndi zina.

Sizitanthauza kuti ngati supanga promote za haram nde kuti luso lako kapena sukhala ndi ma followers ambiri.

Muopeni allah ma content creators nonse musapange promote zinthu za haram.

Source: Voice of islam MALAWI.

29/10/2026

Maa sha Allah . Tiyeni timvele uthenga uwu Ndipo tiyeretse niyyat zathu kuti tiphunzile.
Sheikh Shiraz Abass

Ubwino wa chisilamu ndiumeneu,kulibe zonamizana kuti pelekan seed ayi,chimanenelatu poyela kuti mukazunzikila chinthu nd...
27/10/2026

Ubwino wa chisilamu ndiumeneu,kulibe zonamizana kuti pelekan seed ayi,chimanenelatu poyela kuti mukazunzikila chinthu ndipomwe mudzapeza zokoma,kulibeko za miracle money kulibeko za zisomo zomwe azibusa ena amapezelapo mwai obela nkhosa zopusa,chisilamu chimafanana kwambili ndi chiphunzitso cha bible koma zimasianako ndi chi khristu kamba kakuti atambwali ena amapotoza dala zonena za bible kuti akwanilitse zofuna zawo.

Pomwe bible limati aliese adzadya thukuta lake ndipomwe azibusa ena akuti bweresan thukuta lanu kwaine ndilidye mudzina la seed,chi khristu chinalowa business atambwali anapezelapo mwai.

Wolemba : Ibrahim Swed.

26/10/2026

Sheikh DAITON KAZEMBE.
Akuti azibambo amafunsila.
Tamvelani.

Patuma Shaibu wasankhidwa kuti ndi msungwana wachisilamu amene wasunga Chisilamu komanso kukhala ndi mwambo muzaka zonse...
25/10/2026

Patuma Shaibu wasankhidwa kuti ndi msungwana wachisilamu amene wasunga Chisilamu komanso kukhala ndi mwambo muzaka zonse wakhala akuphunzira pa Mubas.

Anzake onse pa Mubas amusankha iyeyu pomwe amasanzikana, kudya limodzi ndikupasana mphoto mu usiku wadzulo loweruka ku Victoria Garden munzinda wa Blantyre.

Mphotozi zinapita kwa oyenera chifukwa iyeyu akamayenda komanso mmene amalandilira mphotozi Patuma amayang'ana pansi.

Allah amufewetsere Patuma moyo wadziko lino komanso ukudza komanso mpase ntchito yabwino komanso mwamuna wabwino. Allahuma Ameen 🤲

Olemba : Yasin Limu

 Mpikisano owerenga ndi kuloweza Qur’an wayamba pa sukulu ya pulayimale ya Madziamera, mdera la mfumu yaikulu Mposa, m’b...
24/10/2026



Mpikisano owerenga ndi kuloweza Qur’an wayamba pa sukulu ya pulayimale ya Madziamera, mdera la mfumu yaikulu Mposa, m’boma la Machinga.

Mpikisanowu wakonzedwa ndi bungwe la Youngmen’s Islamic Propagation, ndipo mtsogoleri wa bungwe la Islamic Commission for Justice and Freedom, Abdul-Rahman Ajasi, ndiye mlendo wolemekezeka.

Masukulu a madrasa okwana 50 ndi amene akutenga nawo mbali pa mpikisanowu.

Mafumu, ma Sheikh komanso makolo nawonso afika pa mwambowu kudzachitira umboni.

Ana omwe achite bwino pa mpikisanowu alandira mphoto zosiyanasiyana, kuphatikizapo ndalama komanso mabuku Qur’an.

Olemba: Yusuf Daisa.

24/10/2026

SHEIKH ABDUL NOOR FUNDI .
Tilowe chisilamu ndi mtima wonse.

Ndi angati amene takhala tikupereka salaam kwa anthu awa kenako kuzindikila kuli zii osayankhidwa?  awa ndi a postoli. K...
23/10/2026

Ndi angati amene takhala tikupereka salaam kwa anthu awa kenako kuzindikila kuli zii osayankhidwa? awa ndi a postoli. Komabe ena amangoyankha😂

Address

Ngomano Buildings Shop Number 15
Liwonde

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when OSMAN & Family Investment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category