Johnbull zagwa

Johnbull zagwa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Johnbull zagwa, Grocers, Box 65 Mponela Dowa, Lilongwe.

17/12/2025
17/12/2025

Zikanakhala bwino mkazi tikanamabadwa naye ngati nkhunda koma zomafusirana mutakula kalezi aaaaaa ndisaname zimawawa zikavutapa

Ndri ndi mbeu ya chimanga ya mtundu wa bantamu imeneyi bweran dzatigulen 0994000200 pa Mponela
15/11/2025

Ndri ndi mbeu ya chimanga ya mtundu wa bantamu imeneyi bweran dzatigulen 0994000200
pa Mponela

Mtendere wa mumtima umaposa zose phala lamatsukwa lothira juice
26/10/2025

Mtendere wa mumtima umaposa zose phala lamatsukwa lothira juice

22/10/2025

ma bankers mulipo?????

20/10/2025

Azanga akenkelesi president wachipani chathu ndi Dr Lazarus chakwera pakanali pano tisalore kuti ena atigawanitse . kwamene mufuna utsogoleri wachipanichi wait untill then tdzakuvoterani

Address

Box 65 Mponela Dowa
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Johnbull zagwa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category