01/04/2026
Munthu wina osadziwika, anaba galimoto ya mtundu wa KIA Sorento pafupi ndi malo othirira mafuta pa Kudya ndipo amayendetsa galimotoyo mothamanga kwambiri kulowera nseu wa Sanjika.
Ndipo adaomba chipata chili pafupi ndi sanjika, pothawa wakaomba galimoto ina Ford Everest pafupi ndi ofesi za MRA.
Galimoto yobedwayo zuoneka kuti munalinso mwana kumbuyo ndipo info yonse atanene ndiapolisi akuchilomoni amene amutenga munthu akukayikilidwa kuba yo.