ZATI CHANI APA

Call Contact the business

ZATI CHANI APA Music promo
Advertisement
Serious business
Having fun
Breaking news telling

05/10/2026
😱😱😱Anzanga ndi Abale! A Gunde Media, aja omwe akukonza phwando lamayimbidwe la Independence Music Show, alengeza kuti aw...
08/06/2026

😱😱😱
Anzanga ndi Abale!
A Gunde Media, aja omwe akukonza phwando lamayimbidwe la Independence Music Show, alengeza kuti awonjezeraponso S Khrizy pa mndandanda wa anthu odzayimba pa phwandoli.

Poyamba pa mndandandawu panali Crispy Malawi ndi oyimba ena monga Black Missioneries, Anthony Makondetsa, Temwah, Loiso, Zemban Band, Shano Index, Chizmo Njuchi komanso ena ambiri.

Mkulu wa Gunde Media, a Jack Gunde, wati anachiona choyenera kuwonjezera oyimbayu pa mndandandawu, kamba kakuti, S Khrizy ndi m’modzi mwa oyimba omwe akupereka chikoka kwa achinyamata.

Apa, momwe zateremu tsopano, sikutanthawuza kuti Anzanga (gulu ndi anthu okonda nyimbo za S Khrizy ndi anzake omwe amayimba nawo) akakumana maso ndi maso ndi Abale, (gulu ndi anthu okonda nyimbo za Crispy Malawi komanso anzake ena omwe amayimba nawo).

Phwando la Independence Music Show lidzachitika pa 4 July ku Wakawaka mu mzinda wa Lilongwe.
(by Innocent Kumchedwa – Lilongwe:06/06/26)

11/04/2026

hehehe ine zaka wa pass over channel hehehe muli bwanji 😂😂😂

09/01/2026

Zikomo ambuye kwacha 🙏🙏🙏

Address

Blantye
Blantyre

Telephone

+265899029099

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ZATI CHANI APA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ZATI CHANI APA:

Shortcuts

Share

Category